2 Mafumu 22:9 BL92

9 Ndipo Safani mlembiyo anadza kwa mfumu, nambwezera mfumu mau, nati, Anyamata anu anakhuthula ndalama zopereka m'nyumba, nazipereka m'dzanja la anchito akuyang'anira nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 22

Onani 2 Mafumu 22:9 nkhani