2 Mafumu 23:10 BL92

10 Anawaipitsiranso Tofeti, wokhala m'cigwa ca ana a Hinomu; kuti asapitirize mmodzi yense mwana wace wamwamuna kapena wamkazi pamoto kwa Moleki.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:10 nkhani