2 Mafumu 24:12 BL92

12 ndipo Yoyakini mfumu ya Yuda anaturukira kwa mfumu ya Babulo, iye ndi mace, ndi anyamata ace, ndi akalonga ace, ndi adindo ace; mfumu ya Babulo nimtenga caka cacisanu ndi citatu ca ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:12 nkhani