2 Mafumu 24:13 BL92

13 Naturutsa kucotsa komweko cuma conse ca nyumba ya Yehova, ndi cuma ca nyumba ya mfumu, naduladula zipangizo zonse zagolidi adazipanga Solomo mfumu ya Israyeli m'Kacisi wa Yehova, monga Yehova adanena.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:13 nkhani