2 Mafumu 24:16 BL92

16 Ndi anthu amphamvu onse, ndiwo zikwi zisanu ndi ziwiri, ndi amisiri, ndi osula cikwi cimodzi, onsewo acamuna oyenera nkhondo, omwewo mfumu ya Babulo anadza nao andende ku Babulo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:16 nkhani