2 Mafumu 24:17 BL92

17 Ndipo mfumu ya Babulo analonga Mataniya mbale wa atate wace akhale mfumu m'malo mwace, nasanduliza dzina lace likhale Zedekiya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:17 nkhani