2 Mafumu 24:18 BL92

18 Zedekiya anali wa zaka makumi awiri mphambu cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Hamutala mwana wa Yeremiya wa ku Libina.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:18 nkhani