2 Mafumu 24:20 BL92

20 Pakuti mwa mkwiyo wa Yehova zonse zidacitika m'Yerusalemu ndi m'Yuda, mpaka adawataya pamaso pace; ndipo Zedekiya anapandukira mfumu ya Babulo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:20 nkhani