2 Mafumu 25:1 BL92

1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi cinai ca ufumu wace, mwezi wakhumi, tsiku lakhumi la mwezi, Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iye ndi khamu lace lonse anadzera Yerusalemu, naumangira misasa, naumangira timalinga mouzinga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25

Onani 2 Mafumu 25:1 nkhani