2 Mafumu 24:7 BL92

7 Koma mfumu ya Aigupto sinabwerezanso kuturuka m'dziko lace, pakuti mfumu ya Babulo idalanda kuyambira ku mtsinje wa Aigupto kufikira ku mtsinje Firate, ndilo lonse anali nalo mfumu ya Aigupto.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 24

Onani 2 Mafumu 24:7 nkhani