20 Ndipo Nebuzaradani mkuru wa olindirira anawatenga, napita nao kwa mfumu ya Babulo ku Ribila.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 25
Onani 2 Mafumu 25:20 nkhani