2 Mafumu 3:10 BL92

10 Ndipo mfumu ya Israyeli inati, Kalanga ife! pakuti Yehova waitana mafumu ife atatu kutipereka m'dzanja la Moabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:10 nkhani