2 Mafumu 3:26 BL92

26 Ndipo ataona mfumu ya Moabu kuti nkhondo idamlaka, anapita nao anthu mazana asanu ndi awiri akusolola lupanga, kupyola kufikira kwa mfumu ya Edomu, koma sanakhoza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:26 nkhani