2 Mafumu 3:27 BL92

27 Pamenepo anagwira mwana wace wamwamuna woyamba amene akadakhala mfumu m'malo mwace, nampereka nsembe yopsereza palinga. Ndipo anakwiyira Israyeli kwambiri; potero anamcokera, nabwerera ku dziko lao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 3

Onani 2 Mafumu 3:27 nkhani