2 Mafumu 4:22 BL92

22 Naitana mwamuna wace, nati, Nditumizire mmodzi wa anyamata ndi buru mmodzi, kuti ndithamangire kwa munthu uja wa Mulungu, ndi kubweranso.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:22 nkhani