2 Mafumu 4:23 BL92

23 Ndipo anati, Ulikumuka kwa iye lero cifukwa ninji? ngati mwezi wakhala, kapena: mpa sabata? Koma anati, Kuli bwino.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:23 nkhani