2 Mafumu 4:39 BL92

39 Naturuka wina kukachera ndiwo kuthengo, napeza conga ngati mpesa, nacherapo zipuzi kudzaza m'pfunga mwace, nadza, nazicekera-cekera m'nkhali ya cakudya, popeza sanazidziwa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:39 nkhani