2 Mafumu 4:40 BL92

40 Pamenepo anagawira anthu kuti adye. Koma kunali; pakudya cakudyaco, anapfuula nati, Munthu wa Mulungu, muli imfa m'nkhalimo. Ndipo sanatha kudyako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:40 nkhani