2 Mafumu 5:10 BL92

10 Ndipo Elisa anamtumira mthenga, ndi kuti, Kasambe m'Yordano kasanu ndi kawiri, ndi mnofu wako udzabwerera momwe, nudzakhala wokonzeka.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:10 nkhani