2 Mafumu 5:11 BL92

11 Koma Namani adapsa mtima, nacoka, nati, Taona, ndinati m'mtima mwanga, kuturuka adzanditurukira, nadzaima ndi kuitana pa dzina la Yehova Mulungu wace, ndi kuweyula dzanja lace pamalopo, ndi kuciritsa wakhateyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:11 nkhani