2 Mafumu 5:15 BL92

15 Pamer nepo anabwerera kwa munthu wa Mulungu iye ndi gulu lace lonse, nadzaima pamaso pace, nati, Taonani, tsopano ndidziwa kuti palibe Mulungu pa dziko lonse lapansi, koma kwa Israyeli ndiko; ndipo tsopano, mulandire cakukuyamikani naco kwa mnyamata wanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:15 nkhani