16 Koma anati, Pali Yehova, amene ndiima pamaso pace, sindidzalandira kanthu. Ndipo anamkangamiza acilandire, koma anakana.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5
Onani 2 Mafumu 5:16 nkhani