2 Mafumu 5:5 BL92

5 Pamenepo mfumu ya Aramu inati, Tiye, muka, ndidzatumiza kalata kwa mfumu ya Israyeli. Pamenepo anacoka, atatenga siliva: matalente khumi, ndi golidi masekeli zikwi zisanu ndi cimodzi, ndi zobvala zakusintha khumi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:5 nkhani