2 Mafumu 5:6 BL92

6 Ndipo anafika kwa mfumu ya Israyeli ndi kalata, wakuti, Pakulandira kalata uyu, taonani, ndatumiza Namani mnyamata wanga kwa inu, kuti mumciritse khate lace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:6 nkhani