2 Mafumu 5:7 BL92

7 Ndipo kunali atawerenga kalatayu mfumu ya Israyeli, anang'amba zobvala zace, nati, Ngati ndine Mulungu, kupha ndi kubwezera moyo, kuti ameneyo atumiza kwa ine kumciritsa munthu khate lace? pakuti dziwani, nimupenye, kuti alikufuna cifukwa pa ine.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:7 nkhani