2 Mafumu 6:22 BL92

22 Nati, Musawakanthe; kodi mumakantha omwe mwawagwira ndi lupanga ndi uta wanu? apatseni mkate ndi madzi adye namwe, namuke kwa mbuye wao.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:22 nkhani