2 Mafumu 6:23 BL92

23 Ndipo anwakonzera cakudya cambiri, nadya namwa iwo; nawauza amuke; namuka kwa mbuye wao. Ndipo magulu a Aramu sanadzanso ku dziko la Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:23 nkhani