29 Ndipo tinaphika mwana wanga ndi kumudya, ndi mawa wace ndinanena naye, Tenga mwana wako, timudye; koma wambisa mwana wace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6
Onani 2 Mafumu 6:29 nkhani