2 Mafumu 6:30 BL92

30 Ndipo pakumva mfumu mau a mkaziyo, anang'amba zobvala zace alinkupita nayenda palinga, anthu napenya; ndipo taonani, pali ciguduli m'kati pa thupi lace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6

Onani 2 Mafumu 6:30 nkhani