31 Nati iye, Andilange Mulungu naonjezeko, ngati mutu wa Elisa mwana wa Safati uti ukhale pa iye lero lino.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6
Onani 2 Mafumu 6:31 nkhani