33 Akali cilankhulire nao, tapenyani, wamtsikira mthengayo; ndi mfumu inati, Taonani, coipa ici cicokera kwa Yehova; ndilindiranjinso Yehova?
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 6
Onani 2 Mafumu 6:33 nkhani