2 Mafumu 7:1 BL92

1 Ndipo Elisa anati, Mverani mau; a Yehova; atero Yehova, Mawa dzuwa lino adzagula muyeso wa ufa ndi sekeli, adzagulanso miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, pa cipata ca Samariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:1 nkhani