2 Mafumu 7:2 BL92

2 Pamenepo kazembe amene mfumu adafotsamira pa dzanja lace anamyankha munthu wa Mulungu, nati, Taonani, Yehova angacite mazenera m'mwamba cidzacitika ici kodi? Nati iye, Taona, udzaciona ndi maso ako, koma iwe sudzadyako ai.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:2 nkhani