2 Mafumu 7:16 BL92

16 Naturuka anthu, nafunkha m'misasa ya Aaramu. Ndipo anagula miyeso wa ufa ndi sekeli, nagulanso miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, monga umo adanenera Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:16 nkhani