2 Mafumu 7:18 BL92

18 Ndipo kunacitika, monga adanena munthu wa Mulungu kwa mfumu, ndi kuti, Adzagula miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, adzagulanso muyeso wa ufa ndi sekeli; kudzatero mawa, dzuwa lino, pa cipata ca Samariya;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:18 nkhani