2 Mafumu 7:19 BL92

19 ndipo kazembe uja adayankha munthu wa Mulunguyo, nati, Taonani tsono, Yehova angacite mazenera m'mwamba, cikacitika ici kodi? Nati iye, Taona, udzaciona ici ndi maso ako, koma osadyako ai;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:19 nkhani