2 Mafumu 8:1 BL92

1 Ndipo Elisa ananena ndi mkazi uja adamuukitsira mwana wace, kuti, Nyamuka, numuke iwe ndi banja lako, nugonere komwe ukaone malo; pakuti Yehova waitana njala, nidzagwera dziko zaka zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:1 nkhani