2 Mafumu 8:13 BL92

13 Nati Hazaeli, Koma nanga kapolo wanu ali ciani, ndiye garu, kuti akacite cinthu cacikuru ici? Nayankha Elisa, Yehova wandionetsa kuti udzakhala mfumu ya pa Aramu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:13 nkhani