2 Mafumu 8:14 BL92

14 Ndipo anacoka kwa Elisa, nadza kwa mbuye wace; ameneyo ananena naye, Anakuuza ciani Elisa? Nati iye, Anandiuza kuti mudzacira ndithu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:14 nkhani