2 Mafumu 8:16 BL92

16 Ndipo caka cacisanu ca Yoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Israyeli, pokhala Yehosafati mfumu ya Yuda, Yehoramu mwana wa Yehosafati analowa ufumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:16 nkhani