2 Mafumu 8:17 BL92

17 Ndiye wa zaka makumi atatu ndi ciwiri polowa ufumu wace, nacita ufumu zaka zisanu ndi zitatu ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:17 nkhani