2 Mafumu 8:27 BL92

27 Ndipo anayenda m'njira ya nyumba ya Ahabu, nacita coipa pamaso pa Yehova, m'mene inacitira nyumba ya Ahabu; pakuti ndiye wa cibale ca banja la Ahabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:27 nkhani