2 Mafumu 8:28 BL92

28 Ndipo anamuka Yoramu mwana wa Ahabu kukathira nkhondo pa Hazaeli mfumu ya Aramu ku Ramoti Gileadi; ndi Aaramu analasa Yoramu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:28 nkhani