2 Mafumu 9:1 BL92

1 Ndipo Elisa mneneriyo anaitana mmodzi wa ana a aneneri, nanena naye, Udzimangire m'cuuno, nutenge nsupa iyi ya mafuta m'dzanja mwako, numuke ku Ramoti Gileadi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:1 nkhani