2 Mafumu 9:2 BL92

2 Ndipo ukafikako, ukaunguzeko Yehu mwana wa Yehosafati mwana wa Nimsi, nulowe numnyamukitse pakati pa abale ace, nupite naye ku cipinda cam'katimo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:2 nkhani