10 Ndipo agaru adzamudya Yezebeli pa dera la Yezreeli, wopanda wina wakumuika. Pamenepo anatsegula pakhomo, nathawa.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9
Onani 2 Mafumu 9:10 nkhani