2 Mafumu 9:11 BL92

11 Ndipo Yehu anaturukira kwa anyamata a mbuye wace, nanena naye wina, Mtendere kodi? anakudzera cifukwa ninji wamisala uyu? Nanena nao, Mumdziwa munthuyo ndi makambidwe ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:11 nkhani