16 Nayenda Yehu m'gareta, namuka ku Yezreeli, popeza Yoramu anagonako; ndi Ahaziya mfumu ya Yuda anatsikira kukamuona Yoramu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9
Onani 2 Mafumu 9:16 nkhani