2 Mafumu 9:15 BL92

15 koma mfumu Yoramu adabwera ku Yezreeh ampoletse mabala ace anamkantha Aaramu, muja adalimbana naye Hazaeli mfumu ya Aramu. Nati Yehu, Ukatero mtima wanu, asapulumuke mmodzi yense kuturuka m'mudzi kukafotokozera m'Yezreeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:15 nkhani