2 Mafumu 9:19 BL92

19 Pamenepo anatumiza wina wapakavalo, nawafika, nati, Atero mfumu, Mtendere kodi? Nati Yehu, Ngwanji mtendere, tembenukira m'mbuyo mwanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 9

Onani 2 Mafumu 9:19 nkhani